1 Akorinto 4:11 - Buku Lopatulika11 Kufikira nthawi yomwe ino timva njala, timva ludzu, tili amaliseche, tikhomedwa, tilibe pokhazikika; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201411 Kufikira nthawi yomwe yino timva njala, timva ludzu, tili amaliseche, tikhomedwa, tilibe pokhazikika; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa11 Mpaka tsopano lino timamva njala ndi ludzu, ndipo ndife ausiŵa. Anthu akutimenya, ndipo tilibe pokhala penipeni. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero11 Mpaka pano tili ndi njala ndi ludzu, tili ndi sanza, tikuzunzidwa, tilibe nyumba. Onani mutuwo |