1 Akorinto 3:21 - Buku Lopatulika21 Chifukwa chake palibe mmodzi adzitamande mwa anthu. Pakuti zinthu zonse nzanu; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201421 Chifukwa chake palibe mmodzi adzitamande mwa anthu. Pakuti zinthu zonse nzanu; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa21 Nchifukwa chake pasakhale wina aliyense wonyadira anthu chabe. Zinthu zonse nzanu: Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero21 Choncho, wina asanyadire anthu chabe! Zonse ndi zanu, Onani mutuwo |