Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




1 Akorinto 3:20 - Buku Lopatulika

20 ndiponso Ambuye azindikira zolingirira za anzeru, kuti zili zopanda pake.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

20 ndiponso Ambuye azindikira zolingirira za anzeru, kuti zili zopanda pake.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

20 Penanso Malembo akuti, “Ambuye amaŵadziŵa maganizo a anthu anzeru kuti ndi achabe.”

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

20 ndiponso, “Ambuye amadziwa kuti maganizo a wanzeru ndi opandapake.”

Onani mutuwo Koperani




1 Akorinto 3:20
6 Mawu Ofanana  

Aphokoseranji amitundu, nalingiriranji anthu zopanda pake?


Yehova adziwa zolingalira za munthu, kuti zili zachabe.


Kulibe nzeru ngakhale luntha ngakhale uphungu wotsutsana ndi Yehova.


chifukwa kuti, ngakhale anadziwa Mulungu, sanamchitire ulemu wakuyenera Mulungu, ndipo sanamyamike; koma anakhala opanda pake m'maganizo ao, ndipo unada mtima wao wopulukira.


Penyani kuti pasakhale wina wakulanda inu ngati chuma, mwa kukonda nzeru kwake, ndi chinyengo chopanda pake, potsata mwambo wa anthu, potsata zoyamba za dziko lapansi, osati potsata Khristu;


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa