1 Akorinto 3:2 - Buku Lopatulika2 Ndinadyetsa inu mkaka, si chakudya cholimba ai; pakuti simungachithe; ngakhale tsopano lino simungachithe; pakuti mulinso athupi; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20142 Ndinadyetsa inu mkaka, si chakudya cholimba ai; pakuti simunachikhoza; ngakhale tsopano lino simuchikhoza; pakuti mulinso athupi; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa2 Ndidakumwetsani mkaka, osakupatsani chakudya cholimba, chifukwa simukadatha kuchidya. Ngakhalenso tsopano simungathe kuchidya, Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero2 Ndinakupatsani mkaka osati chakudya cholimba pakuti munali musanakonzeke kuchilandira. Zoonadi, simunakonzekebe. Onani mutuwo |