1 Akorinto 3:12 - Buku Lopatulika12 Koma ngati wina amanga pa mazikowo, golide, siliva, miyala ya mtengo wake, mtengo, udzu, dziputu, Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201412 Koma ngati wina amanga pa mazikowo, golide, siliva, miyala ya mtengo wake, mtengo, udzu, dziputu, Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa12 Pa mazikoŵa munthu angathe kumangapo ndi golide, siliva, miyala yamtengowapali, mitengo, udzu kapena mapesi. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero12 Ngati munthu aliyense amanga pa maziko awa pogwiritsa ntchito golide, siliva, miyala yamtengowapatali, milimo yamitengo, tsekera kapena udzu, Onani mutuwo |