1 Akorinto 2:5 - Buku Lopatulika5 kuti chikhulupiriro chanu chisakhale m'nzeru ya anthu, koma mu mphamvu ya Mulungu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20145 kuti chikhulupiriro chanu chisakhale m'nzeru ya anthu, koma mu mphamvu ya Mulungu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa5 Ndinkachita zimenezi kuti chikhulupiriro chanu chisakhazikike pa nzeru za anthu, koma chikhazikike pa mphamvu za Mulungu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero5 kuti chikhulupiriro chanu chisatsamire pa nzeru ya anthu koma pa mphamvu za Mulungu. Onani mutuwo |