1 Akorinto 2:2 - Buku Lopatulika2 Pakuti ndinatsimikiza mtima kuti ndisadziwe kanthu mwa inu, koma Yesu Khristu, ndi Iye wopachikidwa. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20142 Pakuti ndinatsimikiza mtima kuti ndisadziwe kanthu mwa inu, koma Yesu Khristu, ndi Iye wopachikidwa. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa2 Koma ndidaatsimikiza kuti pamene ndili pakati panu, ndiiŵale zina zonse, kupatula Yesu Khristu yekha, koma tsono amene adapachikidwa pa mtanda. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero2 Pakuti ndinatsimikiza pamene ndinali ndi inu kuti ndisadziwe kanthu kena kupatula Yesu Khristu wopachikidwayo. Onani mutuwo |