1 Akorinto 2:10 - Buku Lopatulika10 Koma kwa ife Mulungu anationetsera izi mwa Mzimu; pakuti Mzimu asanthula zonse, zakuya za Mulungu zomwe. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201410 Koma kwa ife Mulungu anationetsera izi mwa Mzimu; pakuti Mzimu asanthula zonse, zakuya za Mulungu zomwe. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa10 Ifeyo Mulungu adatiwululira zimenezi mwa Mzimu Woyera. Pajatu Mzimuyo amadziŵa zinthu zonse kotheratu, ngakhalenso maganizo ozama a Mulungu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero10 koma Mulungu waululira ife mwa Mzimu wake. Mzimu amafufuza zinthu zonse, ndi zozama za Mulungu zomwe. Onani mutuwo |