1 Akorinto 16:3 - Buku Lopatulika3 Ndipo pamene ndifika, ndidzatuma iwo amene mudzawayesa oyenera, ndi makalata, apite nayo mphatso yanu ku Yerusalemu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20143 Ndipo pamene ndifika, ndidzatuma iwo amene mudzawayesa oyenera, ndi akalata, apite nayo mphatso yanu ku Yerusalemu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa3 Tsono ndikadzafika, ndidzaŵapatsa makalata anthu amene mungaŵasankhe, ndipo ndidzaŵatuma kuti akapereke mphatso yanuyo ku Yerusalemu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero3 Pamenepo, ndikadzafika, ndidzawapatsa makalata a umboni anthu amene mudzawasankhe ndi kuwatuma kuti akapereka mphatso zanu ku Yerusalemu. Onani mutuwo |