1 Akorinto 13:6 - Buku Lopatulika6 sichikondwera ndi chinyengo, koma chikondwera ndi choonadi; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20146 sichikondwera ndi chinyengo, koma chikondwera ndi choonadi; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa6 Sichikondwerera zosalungama, koma chimakondwerera choona. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero6 Chikondi sichikondwera ndi zoyipa koma chimakondwera ndi choonadi. Onani mutuwo |