1 Akorinto 13:4 - Buku Lopatulika4 Chikondi chikhala chilezere, chili chokoma mtima; chikondi sichidukidwa; chikondi sichidziwa kudzitamanda, sichidzikuza, Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20144 Chikondi chikhala chilezere, chili chokoma mtima; chikondi sichidukidwa; chikondi sichidziwa kudzitamanda, sichidzikuza, Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa4 Chikondi ncholeza mtima ndiponso nchofatsa. Chikondi chilibe kaduka, ndipo sichidzitamanda kapena kudzikuza. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero4 Chikondi nʼcholeza mtima, chikondi nʼchokoma mtima, chilibe nsanje, sichidzikuza, sichidzitamandira. Onani mutuwo |