Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




1 Akorinto 12:5 - Buku Lopatulika

5 Ndipo pali mautumiki osiyana, koma Ambuye yemweyo.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

5 Ndipo pali mautumiki osiyana, koma Ambuye yemweyo.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

5 Pali njira zosiyanasiyana zotumikira, koma Ambuye amene timaŵatumikira ndi amodzimodzi.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

5 Pali mautumiki osiyanasiyana koma Ambuye yemweyo.

Onani mutuwo Koperani




1 Akorinto 12:5
10 Mawu Ofanana  

Ndipo musatchedwa atsogoleri, pakuti alipo mmodzi Mtsogoleri wanu, ndiye Khristu.


Mau amene anatumiza kwa ana a Israele, akulalikira Uthenga Wabwino wa mtendere mwa Yesu Khristu (ndiye Ambuye wa onse)


Ndipo pali mphatso zosiyana, koma Mzimu yemweyo.


Ndipo pali machitidwe osiyana, koma Mulungu yemweyo, wakuchita zinthu zonse mwa onse.


koma kwa ife kuli Mulungu mmodzi, Atate amene zinthu zonse zichokera kwa Iye, ndi ife kufikira kwa Iye; ndi Ambuye mmodzi Yesu Khristu, amene zinthu zonse zili mwa Iye, ndi ife mwa Iye.


ndi malilime onse avomere kuti Yesu Khristu ali Ambuye, kuchitira ulemu Mulungu Atate.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa