1 Akorinto 12:2 - Buku Lopatulika2 Mudziwa kuti pamene munali amitundu, munatengedwa kunka kwa mafano aja osalankhula, monga munatsogozedwa. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20142 Mudziwa kuti pamene munali amitundu, munatengedwa kunka kwa mafano aja osalankhula, monga munatsogozedwa. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa2 Mukudziŵa kuti pamene munali akunja, anthu ankakusokezani mwa njira izi ndi izi, kukukokerani ku mafano osalankhula. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero2 Inu mukudziwa kuti pamene munali akunja, ankakusocheretsani mʼnjira zosiyanasiyana ndi kukukokerani ku mafano osayankhula. Onani mutuwo |