1 Akorinto 12:1 - Buku Lopatulika1 Koma za mphatso zauzimu, abale, sindifuna kuti mukhale osadziwa. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20141 Koma za mphatso zauzimu, abale, sindifuna kuti mukhale osadziwa. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa1 Abale, ndifuna kuti muzindikire bwino za mphatso za Mzimu Woyera. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero1 Tsopano abale anga okondedwa, sindikufuna mukhale osadziwa za mphatso za Mzimu. Onani mutuwo |