1 Akorinto 11:2 - Buku Lopatulika2 Ndipo ndikutamandani kuti m'zinthu zonse mukumbukira ine, ndi kuti musunga miyambo monga ndinapereka kwa inu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20142 Ndipo ndikutamandani kuti m'zinthu zonse mukumbukira ine, ndi kuti musunga miyambo monga ndinapereka kwa inu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa2 Ndikukuyamikani chifukwa mumandikumbukira pa zonse, ndipo mumasunga miyambo imene ndidakusiyirani. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero2 Ndikukuyamikani chifukwa chondikumbukira pa zonse ndiponso posunga ziphunzitso monga ndinakuphunzitsirani. Onani mutuwo |