1 Akorinto 11:1 - Buku Lopatulika1 Khalani onditsanza ine, monga inenso nditsanza Khristu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20141 Khalani onditsanza ine, monga inenso nditsanza Khristu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa1 Muzinditsanzira ine monga momwe inenso ndimatsanzira Khristu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero1 Tsatirani chitsanzo changa, monga inenso nditsatira chitsanzo cha Khristu. Onani mutuwo |