1 Akorinto 10:8 - Buku Lopatulika8 Kapena tisachite dama monga ena a iwo anachita dama, nagwa tsiku limodzi zikwi makumi awiri ndi zitatu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20148 Kapena tisachite dama monga ena a iwo anachita dama, nagwa tsiku limodzi zikwi makumi awiri ndi zitatu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa8 Tisachite dama monga momwe adaachitira ena mwa iwo: paja pa tsiku limodzi adafa anthu zikwi makumi aŵiri ndi zitatu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero8 Tisachite chigololo monga ena mwa iwo anachitira ndipo tsiku limodzi anafapo anthu 23,000. Onani mutuwo |