1 Akorinto 10:6 - Buku Lopatulika6 Koma zinthu izi zinachitika, zikhale zotichenjeza ife, kuti tisalakalake zoipa ife, monganso iwowo analakalaka. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20146 Koma zinthu izi zinachitika, zikhale zotichenjeza ife, kuti tisalakalake zoipa ife, monganso iwowo analakalaka. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa6 Tsono zimene zidachitikazi ndi zitsanzo zotichenjeza ife, kuti tisamasirira zoipa monga adaachitira iwowo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero6 Tsono zinthu izi zinachitika kuti zikhale chitsanzo, kuti ife tisayike mitima yathu pa zinthu zoyipa monga anachitira makolo athuwo. Onani mutuwo |