1 Akorinto 10:5 - Buku Lopatulika5 Koma ochuluka a iwo Mulungu sanakondwere nao; pakuti anamwazika m'chipululu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20145 Koma ochuluka a iwo Mulungu sanakondwera nao; pakuti anamwazika m'chipululu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa5 Komabe ambirimbiri mwa iwo Mulungu sadakondwere nawo, kotero kuti adafera m'chipululu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero5 Ngakhale zinali choncho, Mulungu sanakondwere ndi ambiri a iwo, motero ambiri mwa iwo anafera mʼchipululu. Onani mutuwo |