1 Akorinto 1:19 - Buku Lopatulika19 Pakuti kulembedwa, Ndidzaononga nzeru za anzeru, ndi kuchenjera kwa ochenjera ndidzakutha. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201419 Pakuti kulembedwa, Ndidzaononga nzeru za anzeru, ndi kuchenjera kwa ochenjera ndidzakutha. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa19 Paja Malembo akuti, “Ndidzaononga nzeru za anthu anzeru, ndidzathetsa kuchenjera kwa anthu ochenjera.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero19 Pakuti kwalembedwa kuti, “Ine ndidzawononga nzeru za anthu anzeru; luntha la anthu aluntha Ine ndidzalinyoza.” Onani mutuwo |