Koma pamene abale ake adakwera kunka kuchikondwerero, pomwepo Iyenso anakwera, si poonekera, koma monga mobisalika.
Yohane 7:9 - Buku Lopatulika Ndipo m'mene adanena nao zimenezi anakhalabe mu Galileya. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Ndipo m'mene adanena nao zimenezi anakhalabe m'Galileya. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Yesu atanena zimenezo, adatsalira m'Galileya. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Atanena izi, Iye anakhalabe mu Galileya. |
Koma pamene abale ake adakwera kunka kuchikondwerero, pomwepo Iyenso anakwera, si poonekera, koma monga mobisalika.
Kwerani inu kunka kuphwando; sindikwera Ine kuphwando ili tsopano apa; pakuti nthawi yanga siinakwanire.