Koma Petro ananyamuka nathamangira kumanda, ndipo powerama anaona nsalu zabafuta pazokha; ndipo anachoka nanka kwao, nazizwa ndi chija chidachitikacho.
Yohane 20:3 - Buku Lopatulika Anatuluka tsono Petro ndi wophunzira winayo, nalinkupita kumanda. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Anatuluka tsono Petro ndi wophunzira winayo, nalinkupita kumanda. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Pamenepo Petro ndi wophunzira wina uja adatuluka napita ku manda. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Choncho Petro ndi wophunzira winayo ananyamuka kupita ku manda. |
Koma Petro ananyamuka nathamangira kumanda, ndipo powerama anaona nsalu zabafuta pazokha; ndipo anachoka nanka kwao, nazizwa ndi chija chidachitikacho.
Koma anathamanga onse awiri pamodzi; ndipo wophunzira winayo anathamanga naposa Petro, nayamba kufika kumanda;