ng'ombe yamphongo imodzi, nkhosa yamphongo imodzi, mwanawankhosa mmodzi wa chaka chimodzi, zikhale nsembe yopsereza;
Numeri 7:64 - Buku Lopatulika tonde mmodzi akhale nsembe yauchimo; Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 tonde mmodzi akhale nsembe yauchimo; Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Adaperekanso tonde mmodzi woperekera nsembe yopepesera machimo. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero mbuzi yayimuna imodzi ya nsembe yopepesera machimo; |
ng'ombe yamphongo imodzi, nkhosa yamphongo imodzi, mwanawankhosa mmodzi wa chaka chimodzi, zikhale nsembe yopsereza;
Ameneyo sanadziwe uchimo anamyesera uchimo m'malo mwathu; kuti ife tikhale chilungamo cha Mulungu mwa Iye.