Numeri 7:60 - Buku Lopatulika Tsiku lachisanu ndi chinai kalonga wa ana a Benjamini, ndiye Abidani mwana wa Gideoni: Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Tsiku lachisanu ndi chinai kalonga wa ana a Benjamini, ndiye Abidani mwana wa Gideoni: Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Tsiku lachisanu ndi chinai linali la Abidani mwana wa Gideoni, mtsogoleri wa Abenjamini. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Pa tsiku lachisanu ndi chinayi Abidani mwana wa Gideoni mtsogoleri wa fuko la Benjamini, anabweretsa chopereka chake. |
chopereka chake ndicho mbale imodzi yasiliva, kulemera kwake masekeli zana limodzi ndi makumi atatu, mbale yowazira imodzi ya masekeli makumi asanu ndi awiri, kuyesa sekeli wa malo opatulika; zonse ziwiri zodzala ndi ufa wosakaniza ndi mafuta, ukhale nsembe yaufa;