Numeri 7:20 - Buku Lopatulika chipande chimodzi chagolide cha masekeli khumi, chodzala ndi chofukiza; Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 chipande chimodzi chagolide cha masekeli khumi, chodzala ndi chofukiza; Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Adaperekanso kambale kamodzi kagolide ka magaramu 110, kodzadza ndi lubani, Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Mbale imodzi yagolide yolemera magalamu 110 yodzaza ndi lubani; |
anabwera nacho chopereka chake mbale imodzi yasiliva, kulemera kwake masekeli zana limodzi ndi makumi atatu, mbale yowazira imodzi yasiliva ya masekeli makumi asanu ndi awiri, kuyesa sekeli wa malo opatulika; zonse ziwiri zodzala ndi ufa wosakaniza ndi mafuta, ukhale nsembe yaufa;
ng'ombe yamphongo imodzi, nkhosa yamphongo imodzi, mwanawankhosa mmodzi wa chaka chimodzi, zikhale nsembe yopsereza;