Ndipo zoyang'anira Eleazara, mwana wa Aroni wansembe, ndizo mafuta a nyaliyo, ndi chofukiza cha fungo lokoma, ndi nsembe yaufa kosalekeza, ndi mafuta odzoza, udikiro wa chihema chonse, ndi zonse zili m'mwemo, malo opatulika, ndi zipangizo zake.
Numeri 4:17 - Buku Lopatulika Ndipo Yehova ananena ndi Mose ndi Aroni, nati, Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Ndipo Yehova ananena ndi Mose ndi Aroni, nati, Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Chauta adauza Mose ndi Aroni kuti, Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Yehova anawuzanso Mose ndi Aaroni kuti, |