Ndipo khamu lonse la ana a Israele linachoka m'chipululu cha Sini, M'zigono zao, monga mwa mau a Yehova, nagona mu Refidimu. Koma kumeneko kunalibe madzi akumwa anthu.
Numeri 33:12 - Buku Lopatulika Nachokera ku chipululu cha Sini, nayenda namanga mu Dofika. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Nachokera ku chipululu cha Sini, nayenda namanga m'Dofika. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Adanyamuka ku chipululu cha Sini, nakamanga mahema ao ku Dofika. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Atachoka ku chipululu cha Sini anakamanga ku Dofika. |
Ndipo khamu lonse la ana a Israele linachoka m'chipululu cha Sini, M'zigono zao, monga mwa mau a Yehova, nagona mu Refidimu. Koma kumeneko kunalibe madzi akumwa anthu.