kufikira Yehova atapumulitsa abale anu, monga anapumulitsa inu, nalandira iwonso dziko limene Yehova Mulungu wanu awapatsa tsidya lija la Yordani; pamenepo mudzabwerera munthu yense ku cholowa chake, chimene ndinakupatsani.
Numeri 32:18 - Buku Lopatulika Sitidzabwerera kwathu, kufikira ana a Israele atalandira yense cholowa chake. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Sitidzabwerera kwathu, kufikira ana a Israele atalandira yense cholowa chake. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Sitidzabwerera kwathu mpaka Mwisraele aliyense atalandira choloŵa chake. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Sitidzabwerera ku midzi yathu mpaka Mwisraeli aliyense atalandira cholowa chake. |