Numeri 3:24 - Buku Lopatulika Ndipo kalonga wa nyumba ya makolo a Ageresoni ndiye Eliyasafu mwana wa Laele. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Ndipo kalonga wa nyumba ya makolo a Ageresoni ndiye Eliyasafu mwana wa Laele. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Eliyasafu mwana wa Laele ndiye anali mtsogoleri wa banja la makolo a Ageresoni. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Mtsogoleri wa mabanja a Ageresoni anali Eliyasafu mwana wa Laeli. |
Ndipo udikiro wa ana a Geresoni m'chihema, chokomanako ndiwo Kachisi, ndi chihema, chophimba chake, ndi nsalu yotsekera pa khomo la chihema chokomanako,