Numeri 26:47 - Buku Lopatulika Iwo ndiwo mabanja a ana aamuna a Asere monga mwa owerengedwa ao, zikwi makumi asanu mphambu zitatu kudza mazana anai. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Iwo ndiwo mabanja a ana amuna a Asere monga mwa owerengedwa ao, zikwi makumi asanu mphambu zitatu kudza mazana anai. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Ameneŵa, anthu okwanira 53,400, ndiwo adaŵerengedwa pa mabanja a Asere. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Awa ndiwo anali mafuko a Aseri. Onse amene anawerengedwa analipo 53,400. |