Mwana wamwamuna wa Dani monga mwa mabanja ake ndiye Suhamu, ndiye kholo la banja la Asuhamu. Iwo ndiwo mabanja a Dani monga mwa mabanja ao.
Numeri 26:43 - Buku Lopatulika Mabanja onse a Asuhamu monga mwa owerengedwa ao ndiwo zikwi makumi asanu ndi limodzi mphambu zinai kudza mazana anai. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Mabanja onse a Asuhamu monga mwa owerengedwa ao ndiwo zikwi makumi asanu ndi limodzi mphambu zinai kudza mazana anai. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Anthu oŵerengedwa pa mabanja onse a Suhamu adakwanira 64,400. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Onse a fuko la Asuhamu amene anawerengedwa analipo 64,400. |
Mwana wamwamuna wa Dani monga mwa mabanja ake ndiye Suhamu, ndiye kholo la banja la Asuhamu. Iwo ndiwo mabanja a Dani monga mwa mabanja ao.