Ana a Giliyadi ndiwo: Iyezere, ndiye kholo la banja la Aiyezere; Heleki, ndiye kholo la banja la Aheleki;
Numeri 26:31 - Buku Lopatulika ndi Asiriele, ndiye kholo la banja la Aasiriele; ndi Sekemu, ndiye kholo la banja la Asekemu; Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 ndi Asiriele, ndiye kholo la banja la Aasiriele; ndi Sekemu, ndiye kholo la banja la Asekemu; Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Ndipo Asiriele anali kholo la banja la Aasiriele. Sekemu anali kholo la banja la Asekemu. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero kuchokera mwa Asirieli, fuko la Aasirieli; kuchokera mwa Sekemu, fuko la Asekemu; |
Ana a Giliyadi ndiwo: Iyezere, ndiye kholo la banja la Aiyezere; Heleki, ndiye kholo la banja la Aheleki;
ndi Semida, ndiye kholo la banja la Asemida; ndi Hefere, ndiye kholo la banja la Ahefere.