Numeri 26:27 - Buku Lopatulika Iwo ndiwo mabanja a Zebuloni monga mwa owerengedwa ao, zikwi makumi asanu ndi limodzi mphambu mazana asanu. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Iwo ndiwo mabanja a Zebuloni monga mwa owerengedwa ao, zikwi makumi asanu ndi limodzi mphambu mazana asanu. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Ameneŵa, anthu okwanira 60,500, ndiwo anali a m'mabanja a Zebuloni, amene adaŵerengedwa. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Awa ndiwo anali mafuko a Zebuloni. Amene anawerengedwa analipo 60,500. |