Numeri 26:25 - Buku Lopatulika Iwo ndiwo mabanja a Isakara monga mwa owerengedwa ao; zikwi makumi asanu ndi limodzi mphambu zinai kudza mazana atatu. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Iwo ndiwo mabanja a Isakara monga mwa owerengedwa ao; zikwi makumi asanu ndi limodzi mphambu zinai kudza mazana atatu. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Ameneŵa, anthu okwanira 64,300, ndiwo anali a m'mabanja a Isakara, amene adaŵerengedwa. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Awa ndi amene anali a fuko la Isakara. Amene anawerengedwa analipo 64,300. |