Pamenepo akalonga a Mowabu ananyamuka, nafika kwa Balaki, nati Alikukana Balamu kudza nafe.
Numeri 22:15 - Buku Lopatulika Koma Balaki anaonjeza kutumanso akalonga, ochuluka, ndi omveka koposa awa. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Koma Balaki anaonjeza kutumanso akalonga, ochuluka, ndi omveka koposa awa. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Balaki adatumanso akalonga ochuluka ndi olemekezeka kopambana oyamba aja. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Kenaka Balaki anatumanso akuluakulu ena ambiri ndi olemekezeka kwambiri kuposa oyamba aja ndipo |
Pamenepo akalonga a Mowabu ananyamuka, nafika kwa Balaki, nati Alikukana Balamu kudza nafe.
Ndipo anadza kwa Balamu, nati kwa iye, Atero Balaki mwana wa Zipori, Pasakhaletu chinthu chakukuletsa kudza kwa ine;