Numeri 22:13 - Buku Lopatulika Ndipo Balamu anauka m'mawa, nati kwa akalonga a Balaki, Mukani ku dziko lanu; popeza Yehova andikaniza kuti ndisapite nanu. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Ndipo Balamu anauka m'mawa, nati kwa akalonga a Balaki, Mukani ku dziko lanu; popeza Yehova andikaniza kuti ndisapite nanu. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Tsono Balamu adadzuka m'maŵa, naŵauza akalonga a Balaki aja kuti, “Bwererani ku dziko lakwanu, pakuti Chauta sadandilole kuti ndipite nanu.” Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Mmawa mwake Balaamu anadzuka ndi kuwuza akuluakulu a Balaki aja kuti, “Bwererani ku dziko la kwanu chifukwa Yehova sanandilole kuti ndipite nanu.” |
Pamenepo akalonga a Mowabu ananyamuka, nafika kwa Balaki, nati Alikukana Balamu kudza nafe.
Ndipo Yehova Mulungu wanu sanafune kumvera Balamu; koma Yehova Mulungu wanu anakusandulizirani tembererolo likhale mdalitso, popeza Yehova Mulungu wanu anakukondani.