chitsime adakumba mafumu, adachikonza omveka a anthu; atanena mlamuli, ndi ndodo zao. Ndipo atachoka kuchipululu anamuka ku Matana;
Numeri 21:19 - Buku Lopatulika atachoka ku Matana ku Nahaliyele; atachoka ku Nahaliyele ku Bamoti; Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 atachoka ku Matana ku Nahaliyele; atachoka ku Nahaliyele ku Bamoti; Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa kuchokera ku Matana adafika ku Nahaliyele, kuchokera ku Nahaliyele adafika ku Bamoti. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Kuchoka ku Matana anapita ku Nahalieli, kuchoka ku Nahalieli anapita ku Bamoti, |
chitsime adakumba mafumu, adachikonza omveka a anthu; atanena mlamuli, ndi ndodo zao. Ndipo atachoka kuchipululu anamuka ku Matana;
atachoka ku Bamoti ku chigwa chili m'dziko la Mowabu, ku mutu wa Pisiga, popenyana ndi chipululu.
Hesiboni ndi mizinda yake yonse yokhala pachidikha; Diboni, ndi Bamoti-Baala ndi Bete-Baala-Meoni;