nimuikemo moto, muikenso chofukiza pamenepo, pamaso pa Yehova, mawa; ndipo kudzali kuti amene Yehova amsankha, wopatulika ndiye; mwakula mphamvu, inu ana a Levi.
Numeri 16:8 - Buku Lopatulika Ndipo Mose ananena ndi Kora, Tamvani tsono, inu ana a Levi; Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Ndipo Mose ananena ndi Kora, Tamvani tsono, inu ana a Levi; Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Mose adauza Kora kuti, “Imvani tsono inu Alevi. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Mose anawuzanso Kora kuti, “Inu Alevi, tsopano tamverani! |
nimuikemo moto, muikenso chofukiza pamenepo, pamaso pa Yehova, mawa; ndipo kudzali kuti amene Yehova amsankha, wopatulika ndiye; mwakula mphamvu, inu ana a Levi.
kodi muchiyesa chinthu chaching'ono, kuti Mulungu wa Israele anakusiyanitsani ku gulu la Israele, kukusendezani pafupi pa Iye, kuchita ntchito ya chihema cha Yehova, ndi kuima pamaso pa khamu kuwatumikira;
Ndipo Mika anamninkha zansembe Mleviyo, ndi mnyamatayo anakhala wansembe wake, nakhala m'nyumba ya Mika.