Ndipo kunali, posonkhanidwa khamulo kutsutsana nao Mose ndi Aroni, kuti anacheukira chihema chokomanako; taonani, mtambo unachiphimba, ndi ulemerero wa Yehova unaoneka.
Numeri 16:43 - Buku Lopatulika Ndipo Mose ndi Aroni anadza kukhomo kwa chihema chokomanako. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Ndipo Mose ndi Aroni anadza kukhomo kwa chihema chokomanako. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Mose ndi Aroni adabwera patsogolo pa chihema chamsonkhano, Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Pamenepo Mose ndi Aaroni anapita patsogolo pa tenti ya msonkhano ija |
Ndipo kunali, posonkhanidwa khamulo kutsutsana nao Mose ndi Aroni, kuti anacheukira chihema chokomanako; taonani, mtambo unachiphimba, ndi ulemerero wa Yehova unaoneka.