Ndipo wansembe mwana wa Aroni azikhala ndi Alevi, polandira Alevi limodzilimodzi la magawo khumi; ndi Alevi azikwera nalo limodzi la magawo khumi mwa limodzilimodzi la magawo khumi kunyumba ya Mulungu wathu, kuzipinda, kunyumba ya chuma.
Numeri 15:19 - Buku Lopatulika kudzali, pakudya inu mkate wa m'dzikolo, muzikwezera Yehova nsembe yokweza. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 kudzali, pakudya inu mkate wa m'dzikolo, muzikwezera Yehova nsembe yokweza. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa ndipo mukamadzadya buledi wam'dzikolo, mudzapereke nsembe kwa Chauta. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero ndipo mukakadya chakudya cha mʼdzikolo, mukapereke gawo lina kwa Yehova monga chopereka. |