Kudzatero ndi ng'ombe iliyonse, kapena nkhosa yamphongo iliyonse, kapena mwanawankhosa aliyense, kapena mwanawambuzi aliyense.
Numeri 15:12 - Buku Lopatulika Monga mwa kuwerenga kwake kwa izi muzikonza, muzitero ndi yonse monga mwa kuwerenga kwake. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Monga mwa kuwerenga kwake kwa izi muzikonza, muzitero ndi yonse monga mwa kuwerenga kwake. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Zingachuluke chotani nyama zoperekedwazo, muchite choncho ndi nyama iliyonse, mpaka zonse kutha. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Ngakhale zingachuluke chotani, chitani izi kwa iliyonse ya nyamazo. |
Kudzatero ndi ng'ombe iliyonse, kapena nkhosa yamphongo iliyonse, kapena mwanawankhosa aliyense, kapena mwanawambuzi aliyense.
Onse akubadwa m'dzikomo achite izi momwemo, pobwera nayo kwa Yehova nsembe yamoto ya fungo lokoma.