Ndipo anadalitsa iwo tsiku lomwelo, nati, Mwa iwe Israele adzadalitsa, kuti, Mulungu akuyese iwe monga Efuremu ndi monga Manase; ndipo anaika Efuremu woyamba wa Manase.
Numeri 13:11 - Buku Lopatulika Wa fuko la Yosefe, wa fuko la Manase, Gadi mwana wa Susi. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Wa fuko la Yosefe, wa fuko la Manase, Gadi mwana wa Susi. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa M'fuko la Yosefe (ndiye kuti m'fuko la Manase) adatuma Gadi mwana wa Susi. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero kuchokera ku fuko la Manase (fuko la Yosefe), Gadi mwana wa Susi; |
Ndipo anadalitsa iwo tsiku lomwelo, nati, Mwa iwe Israele adzadalitsa, kuti, Mulungu akuyese iwe monga Efuremu ndi monga Manase; ndipo anaika Efuremu woyamba wa Manase.