Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Numeri 13:11 - Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

11 kuchokera ku fuko la Manase (fuko la Yosefe), Gadi mwana wa Susi;

Onani mutuwo Koperani

Buku Lopatulika

11 Wa fuko la Yosefe, wa fuko la Manase, Gadi mwana wa Susi.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

11 Wa fuko la Yosefe, wa fuko la Manase, Gadi mwana wa Susi.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

11 M'fuko la Yosefe (ndiye kuti m'fuko la Manase) adatuma Gadi mwana wa Susi.

Onani mutuwo Koperani




Numeri 13:11
4 Mawu Ofanana  

Tsono iye anawadalitsa tsiku limenelo nati, “Aisraeli adzagwiritsa ntchito dzina lanu podalitsa nadzati: Mulungu akudalitseni monga Efereimu ndi Manase.” Choncho anayika Efereimu patsogolo pa Manase.


kuchokera ku fuko la Zebuloni, Gadieli mwana wa Sodi;


kuchokera ku fuko la Dani, Amieli mwana wa Gemali;


Uma, Afeki ndi Rehobu. Mizinda yonse inalipo 22 pamodzi ndi midzi yake.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa