Ana a Sefatiya, mazana atatu mphambu makumi asanu ndi awiri kudza awiri.
A banja la Sefatiya 372.
Zidzukulu za Sefatiya 372
Ndi wa ana a Sefatiya, Zebadiya mwana wa Mikaele; ndi pamodzi naye amuna makumi asanu ndi atatu.
Ana a Ara, mazana asanu ndi limodzi mphambu makumi asanu kudza awiri.
ana a Parosi zikwi ziwiri mphambu zana limodzi kudza makumi asanu ndi awiri.