Ezara 2:4 - Buku Lopatulika4 Ana a Sefatiya, mazana atatu mphambu makumi asanu ndi awiri kudza awiri. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20144 Ana a Sefatiya, mazana atatu mphambu makumi asanu ndi awiri kudza awiri. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa4 A banja la Sefatiya, 372. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero4 zidzukulu za Sefatiya 372 Onani mutuwo |