Nehemiya 7:8 - Buku Lopatulika8 ana a Parosi zikwi ziwiri mphambu zana limodzi kudza makumi asanu ndi awiri. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20148 ana a Parosi zikwi ziwiri mphambu zana limodzi kudza makumi asanu ndi awiri. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa8 A banja la Parosi 2,172. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero8 Zidzukulu za Parosi 2,172 Onani mutuwo |