Nehemiya 7:10 - Buku Lopatulika Ana a Ara, mazana asanu ndi limodzi mphambu makumi asanu kudza awiri. Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Ana a Ara, mazana asanu ndi limodzi mphambu makumi asanu kudza awiri. Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa A banja la Ara 652. Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero Zidzukulu za Ara 652 |
Pakuti ambiri mu Yuda analumbirirana naye chibwenzi; popeza ndiye mkamwini wake wa Sekaniya mwana wa Ara; ndi mwana wake Yehohanani adadzitengera mwana wamkazi wa Mesulamu mwana wa Berekiya.
Ana a Pahatimowabu, a ana a Yesuwa ndi Yowabu, zikwi ziwiri mphambu mazana asanu ndi atatu kudza khumi limodzi ndi asanu ndi atatu.