Baibulo la pa intaneti

Zotsatsa


Baibulo lonse Chipangano Chakale Chipangano Chatsopano




Nehemiya 6:4 - Buku Lopatulika

Nanditumizira ine mau otere kanai; ndinawabwezeranso mau momwemo.

Onani mutuwo

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

Nanditumizira ine mau otere kanai; ndinawabwezeranso mau momwemo.

Onani mutuwo

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

Tsono adanditumizira mau okhaokhawo kanai konse, ndipo ndidaŵayankha chimodzimodzi.

Onani mutuwo

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

Ananditumizira uthenga umodzimodzi omwewu kanayi ndipo ndinawayankha chimodzimodzi.

Onani mutuwo



Nehemiya 6:4
10 Mawu Ofanana  

Ndipo ndinawatumizira mithenga, ndi kuti, Ndilikuchita ntchito yaikulu, sindingathe kutsika; ndiidulirenji padera ntchito poileka ine, ndi kukutsikirani?


Pamenepo Sanibalati anatuma mnyamata wake kwa ine kachisanu, ndi kalata yosatseka m'dzanja mwake;


Wachibwana akhulupirira mau onse; koma wochenjera asamalira mayendedwe ake.


Amkakamiza ndi kukoka kwa mau ake, ampatutsa ndi kusyasyalika kwa milomo yake.


koma chifukwa cha kundivuta ine mkazi wamasiye amene ndidzamweruzira mlandu, kuti angandilemetse ndi kudzaidza kwake.


Chifukwa chake, abale anga okondedwa, khalani okhazikika, osasunthika, akuchuluka mu ntchito ya Ambuye, nthawi zonse, podziwa kuti kuchititsa kwanu sikuli chabe mwa Ambuye.


Koma sitidawafumukire mowagonjera ngakhale ora limodzi; kuti choonadi cha Uthenga Wabwino chikhalebe ndi inu.


Pamenepo Delila anati kwa Samisoni, Taona, wandipusitsa, ndi kundiuza mabodza; undiuze tsopano, ndikupempha, chimene angakumange nacho.


Pamenepo Delila anati kwa Samisoni, Ndikupempha, undiuze umo muchokera mphamvu yako yaikulu, ndi chimene angakumange nacho, kuti akuzunze.