Nehemiya 2:9 - Buku Lopatulika
Ndinafika tsono kwa ziwanga za tsidya lino la mtsinje, ndipo ndinawapatsa makalata a mfumu. Koma mfumu idatumiza apite nane akazembe a nkhondo, ndi apakavalo.
Onani mutuwo
Ndinafika tsono kwa ziwanga za tsidya lino la mtsinje, ndipo ndinawapatsa akalata a mfumu. Koma mfumu idatumiza apite nane akazembe a nkhondo, ndi apakavalo.
Onani mutuwo
Choncho ndidanyamuka ulendo nkukafika kwa abwanamkubwa a chigawo cha Patsidya pa Yufurate, ndipo ndidaŵapatsa makalata a mfumu aja. Monsemo nkuti mfumu itatumiza akulu ankhondo ndiponso anthu okwera pa akavalo, kuti atsakane nane.
Onani mutuwo
Choncho ndinanyamuka ulendo wanga ndipo ndinafika kwa abwanamkubwa a chigawo cha Patsidya pa Yufurate ndipo ndinawapatsa makalata a mfumu. Mfumu nʼkuti itatumiza akulu ankhondo ndi okwera pa akavalo kuti atsagane nane.
Onani mutuwo