Mateyu 7:9 - Buku Lopatulika Kapena munthu ndani wa inu, amene pompempha mwana wake mkate, adzampatsa mwala? Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014 Kapena munthu ndani wa inu, amene pompempha mwana wake mkate, adzampatsa mwala? Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa Ndani mwa inu, mwana wake atampempha buledi, iye nkumupatsa mwala? Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero “Ndani mwa inu, mwana wake akamupempha buledi amamupatsa mwala? |
pakuti yense wakupempha alandira; ndi wakufunayo apeza; ndi kwa wogogodayo chitsegulidwa.